Apolisi mu mzinda wa Blantyre amanga yemwe anali mtolankhani wakale wa Malawi24 McMillan Mhone, kamba ka nkhani yomwe inalembedwa yokhudza munthu woganiziridwa katangale a Abdul Karim Batatawala chaka chatha. Pa 15 August chaka chatha, Malawi24 idatulutsa nkhani yomwe imakamba zambiri zokhudza momwe a Batatawala akuganizilidwira kuti anaphwanya malamulo kuti apeze ma kontalakiti ndi boma la […]
The post Mtolankhani wakale wa Malawi24 wamangidwa kamba ka nkhani yokhudza oganizilidwa katangale Batatawala appeared first on Malawi 24.