Phungu wa mdera la Chikwawa West a Susan Dossi athokoza boma la a Lazarus Chakwera chifukwa chofuna kumanga nsewu wa Chapananga omwe wakhala nthawi yayitali utawonongeka. A Dossi awuza Malawi24 potsatira zomwe adayankhula mtsogoleri wadziko lino a Chakwera ku mtundu wa a Malawi ku nyumba yamalamulo pankhani yofuna kukonza nsewu wa Chapananga omwe adati ukadzatha […]
The post Phungu wa Chikwawa West wathokoza boma chifukwa chofuna kumanga nsewu wa Chapananga appeared first on Malawi 24.