Mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera ati ndi nthawi yabwino tsono kuti makolo azindikire za ubwino okhala ndi ana omwe akhoza kukwanitsa kuwasamala komanso kuwaphunzitsa ndipo ati maphunzilo kuti ayende bwino akuyambila pa zipangizo, ma kalasi abwino, aphunzitsi okwanila komanso kuphatikiza udindo omwe makolo ali nawo. Poyankhula pa sukulu ya pulayimale ya Chikololere ku […]
The post Osangolimbikira kubeleka ana oti simungawasamale — Chakwera appeared first on Malawi 24.