Mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus McCarthy Chakwera watsimikizira mtundu wa a Malawi kuti palibe ngakhale munthu m’modzi yemwe amwalire chifukwa cha njala yomwe yafika posauzana m'madera ambiri m'dziko muno. A Chakwera amayankhula izi Lachitatu pa 21 February, 2024 pomwe anakaonekera m'nyumba ya malamulo momwe anapita kukayankha mafuso okhudza zinthu zosiyanasiyana makamaka zomwe zikukhudza miyoyo […]
The post Palibe yemwe afe ndinjala – atelo a Chakwera appeared first on Malawi 24.