Dziko la Malawi pamodzi ndi mayiko ena onse padziko lapansi lachiwiri pa 13 Febuluwale limakumbukira nawo tsiku la 'Condom' pamene akatswiri ati a Malawi ambiri sakutha kupeza mwayi wa makondomu mwachangu. M'modzi mwa katswili owona za kulera ndi uchembele wabwino yemwenso ndi mkulu wa Family Planning and Association of Malawi (FPAM) Donald Makwakwa awuza wailesi […]
The post Dziko la Malawi silikugwiritsa ntchito kwambiri makondomu appeared first on Malawi 24.