Phungu wa wa dela la ku mmwela cha kum'mawa m'boma la Salima a Mike Ng'ombe Mwawa awatulutsa m'nyumba ya malamulo ndipo ati adzabwere pa 13 malichi kamba ka kuyankhula zosayenera mnyumba ya malamulo mu zokambilana za dzulo. Sipikala wa nyumbayi a Catherine Gotani Hara wati atakamvetsela zomwe a Mwawa anayankhula kudzela pa zotepedwa za m'nyumbayi […]
The post A Mike Mwawa alandila chilango mnyumba ya malamulo nthawi yothaitha appeared first on Malawi 24.