Atatsanzika Mark Harrison, timu ya mpira wa miyendo ya Mighty Mukuru Wanderers tsopano yalemba mphunzitsi watsopano ophunzitsa osewera mu timuyi yemwenso anaphunzitsapo timu ya Nyasa Big Bullets Nsanzurwimo Ramadhan yemwe kwawo ndi ku Burundi. Malingana ndi Chikalata chomwe chatuluka lero pa 14 febuluwale chotsimikizidwa ndi amene anali wa pampando wa olemba ntchito anthuwa a Tiya […]
The post Wanderers yalemba mphunzitsi wakale wa Bullets appeared first on Malawi 24.