A Timothy Mtambo omwe ndi mtsogoleri wa bungwe la Citizens for Transformation (CFT) ati mchitidwe wochita ziwawa pa nkhani za ndale ukuyenera utheletu mdziko muno. Izi ndi malingana ndi kalata yomwe bungwe la CFT latulutsa yomwe wasainira ndi Mtambo, yemwe wadzudzula mtopola omwe anthu ana anachita Loweluka lapitali pomwe anasokoneza komaso kuvulaza otsatira chipani cha […]
The post Mtambo wadzudzula kumenyana pa ndale appeared first on Malawi 24.