Pomwe kudzigulira mavoti pa chisankho cha chaka cha mawa kuli mkati, m’mawa wa Lachinayi kunali “taonani taonani, zilikotu ziliko” mu mzinda wa Lilongwe pomwe aphungu awiri a chipani cha Malawi Congress (MCP) aliyese anagula bokosi la maliro a munthu m’modzi. Nkhaniyi ikuti munthu wina yemwe ndiochokera kudera la kum’mwera cha kum’mawa kwa boma la Lilongwe […]
The post 2025 ationetsa zinthu: aphungu a MCP agula mabokosi awiri a maliro amodzi appeared first on Malawi 24.