Bambo wazaka 50 a Chiyipila Nsato, ali m'manja mwa apolisi ku Lilongwe kaamba kowaganizira kuti iwo ndi anthu ena atatu anakaba nawo katundu okwana 90 miliyoni kwacha ku likulu la tsopano la Radio Maria. Mneneri wa apolisi mchigawo chapakati, a Foster Benjamin, atsimikiza zankhaniyi ndipo iwo atinso pakadali pano akwanitsa kupezapo zipangizo zina kuphatikizapo ma […]
The post Chiyipila Nsato ali m'manja mwa apolisi kamba kogwinya katundu ku wayilesi ya Radio Maria appeared first on Malawi 24.