…akuti “a Malondera analemba zigawenga” Ya pa chiweniweni: phungu wa chipani cha MCP ku Dedza, a Willard Gwengwe omwe bokosi la maliro lomwe anagula lakanidwa mochititsa manyazi, aloza chala phungu nzawo wa chipanichi a Steven Baba Malondera kuti ndiye gwero la zonsezi ndipo akuti phungu nzawoyu sapambana chaka cha mawa chifukwa anthu asiya kuwakonda. A […]
The post Mabokosi awiri maliro amodzi: Gwengwe waloza chala Malondera appeared first on Malawi 24.