Katswiri pa kapezedwe ka chakudya dziko wati ndondomeko ya chuma ya chaka cha 2024/25 ikuyenela kuthandizira ulimi wa mthilila m'dziko muno pofuna kuthana ndi mavuto omwe adza kamba ka ng'amba yomwe yakhudza dziko lino. Ronald Chilumpha, katswiri pa kapezekedwe ka chakudya chokwanila m'dziko muno, wati ndondomekoyi ikuyenela kukhala ndi mayankho okhazikika ku vuto la njala […]
The post Ndondomeko ya chuma cha dziko lino ikuyenera kuthana ndi vuto la njala, atero akatswiri appeared first on Malawi 24.