Pamene dziko lino lili pa mpanipani kusaka ndalama loti ntchito za magetsi zikhale zolongosoka, nduna yatsopano yoona za mphamvu za magetsi a Ibrahim Matola wauza bungwe la Escom kuti liyambilenso kupeleka ndalama kwa matimu a mpira ati ndi cholinga chothana ndi matenda a mu ubongo. Polankhula pamene anakumana ndi ogwila ntchito ku bungweli limene lakhala […]
The post Yambani kupeleka ndalama ku mpira kuti tithane ndi misala – nduna yauza a Escom appeared first on Malawi 24.