Yemwe akufuna kudzayimira chipani cha Democratic Progressive m'dera la Zomba Thondwe pachisankho chakunyumba yamalamulo mi chaka cha 2025 a Dumisani Lindani ati mosakayika konse iwo akudzapambana chisankhocho. A Lindani awuza Malawi24 kuti pakali pano anthu a mdera la Zomba Thondwe akuchikonda chipani cha DPP pamodzi ndi mtsogoleri wachipanichi Professor Peter Muthalika ndipo anthu ambiri ndiwomwe […]
The post Anthu akudikila kuti adzasankhe ine, atero a shado a ku Zomba Thondwe appeared first on Malawi 24.