Mneneri Shepherd Bushiri yemwe ndi tsogoleri wa mpingo wa ECG-The Jesus Nation, wati pomwe lafika vuto la njala mdziko muno, ndipofunika kuti azipembedzo komaso anthu andale ayiwale kaye zakusiyana kwawo pa zikhulupiliro komanso pandale ndikuyamba kuthandiza a Malawi omwe akugona kumimba kukulira malikhweru. Mneneri Bushiri walankhula izi Lamulungu kwa Mkando m'boma la Mulanje komwe anapita […]
The post Bushiri wapempha mgwirizano pa ntchito yothandiza ovutika appeared first on Malawi 24.