Mfumu Makungula a mdera la T/A Nkagula Boma la Zomba akuyimba lokoma pakhomo pawo chifukwa akupha makwacha ndi ng'ombe za mkaka komanso nkhuku za mazira zomwe amaweta. Poyankhula ndi Malawi24, GVH Makungula adati alindi ng'ombe zisanu ndi zitatu za mkaka ndiponso nkhuku ndipo mwezi uliwonse amatolera ndalama zotsachepera 2 million kwacha za mkaka komanso madzira. […]
The post GVH Makungula akuyimba lokoma chifukwa cha ng'ombe za mkaka komanso nkhuku za mazira appeared first on Malawi 24.