Yemwe anali m'modzi mwa akulu akulu ku chipani cha Democratic Progressive DPP a Uladi Mussa ndipo pakali pano adalowa chipani cha Malawi Congress (MCP) ati iwo atafatsa kuwelenga malamulo a chipanichi tsopano ali ndi mangongolomela okapikisana nawo pa mipando iwiri ku msonkhano waukulu omwe chipani cha MCP chipangitse. Poyankhula pa wailesi ya kanema wa Times […]
The post Mlendo Uladi Mussa akapikisana nawo pa mipando iwiri ku MCP appeared first on Malawi 24.