Mtsikana wina wa zaka 17, Mercy Phiri, wafa atawombedwa ndi mphenzi kwa Khosolo madzulo a pa 18 February, 2024 m'boma la Mzimba. M'neneri wa polisi ya Jenda Macfarlen Mseteka wati womwalirayo ndi Mercy Phiri ndipo akuti patsikulo anakumana ndingoziyo atapita kwa amalume ake pamene mphepo ya mkuntho ndi mvula inagwa. Chifukwa cha mantha anaima pakona la […]
The post Mphenzi yapha mtsikana ku Mzimba appeared first on Malawi 24.