Njonda ina yazaka 30 zakubadwa, yapulumukira mkamwa mwa njovu pamene bwalo lamilandu ku Kasungu lamupeza osalakwa pa mlandu omwe amamuzenga ogonana ndi mtsikana yemwe amati ndi wa zaka 16. Mkuluyu yemwe dzina lake ndi Lameck Banda, ananjatidwa kamba koganizilidwa kuti anagonana ndi mtsikanayu ndi kumupatsa pathupi kutsatira ndi momwe makolo amtsikanayu anakamang'alira kuti ndi wa […]
The post Wapulumuka pamene khoti lati msungwana amati anagona nayeyo simwana appeared first on Malawi 24.