Mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera ati mu chaka cha 2024 ndikofunika kukankha kuti zinthu ziyende bwino ndipo wachenjeza kuti kukankha kwina ndikuchotsa anthu omwe akungowononga ndalama mu maofesi aboma. A Chakwera amayankhula izi pa 31 Disembala, 2023 mu uthenga wake womaliza wa mu chaka cha 2023 pomweso anafunila a Malwi chaka chopambana cha […]
The post Mu 2024 tikankhe, atero a Chakwera appeared first on Malawi 24.