Phungu wa nyumba ya malamulo wa dera la kumpoto m'boma la Balaka olemekezeka a Tony Ngalande ati ndi Khumbo lawo kuthandizira kutukula masewero osiyanasiyana pakati pa achinyamata komanso ophunzira msukulu za pulayimale. A Ngalande ayankhula izi lachisanu pamene amakhazikitsa chikho cha mpikisano wa mpira wa miyendo komanso manja chomwe ma timu ochokera msukulu zosiyanasiyana m'boma […]
The post Tony Ngalande akhazikitsa mpikisano wa masewero msukulu za pulayimale appeared first on Malawi 24.