Tsopano mayendedwe akhala wovutirapo pa msewu wa M5 pamene madzi ochuluka adula msewuwu, omwe umatchedwanso kuti Lakeshore, kamba ka mvula yamphamvu yomwe yakhala ikugwa. Msewu umenewu waduka pa malo otchedwa Mwalawoyera kuchokera pa Salima Turn Off kupita ku Salima. Malingana ndi a Portia Kajanga omwe ndi ofalitsa nkhani za bungwe la Roads Authority, izi zili […]
The post Msewu wa Lakeshore waduka appeared first on Malawi 24.