Bungwe lolemba nzika la National Registration Bureau (NRB) lati silisinthila a Malawi omwe akufuna kusinthitsa tsiku lobadwa chifukwa tsiku lobadwa pa chiphaso cha nzika ndilotetezedwa. M'malingana ndi chikalata chomwe bungweli latulutsa pa 19 febuluwale chotsimikidwa ndi mlembi wamkulu wa NRB a Mphatso Sambo, ati bungweli ndilokhudzika ndi kuchuluka kwa anthu amene akusintha tsiku lobadwa pa […]
The post Sitikusinthirani tsiku lobadwa pa chiphaso — NRB appeared first on Malawi 24.