Ngati njira imodzi yokondwelera nyengo ya khilisimisi komanso chaka chatsopano, gulu la pa tsamba la mchezo la WhatsApp la 'Malawian Gossip and Scandals' linakachezela odwala pa chipatala chachikulu cha boma la Salima. Gululi lapereka katundu osiyanasiyana wa ndalama pafupifupi K500 sauzande kwa ana omwe agonekedwa pa chipatalachi ndipo akulandira thandizo la mankhwala. Poyankhula atapereka thandizoli, […]
The post Gulu la pa tsamba la mchezo lathandiza odwala pa chipatala cha Salima appeared first on Malawi 24.