M'modzi wa anthu omwe akufuna utsogoleri ku chipani cha DPP a Dalitso Kabambe awuza mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera kuti ayambe kulongedza popeza kuthekera kokonza zinthu alibe. Malingana ndi a Kabambe omwe anakhalapo mkulu wa bank yaikilu ya Reserve, iwo ali okonzeka kuzakonza zinthu m'dziko muno. Mukulemba kwawo pa tsamba la mchezo m'mawa […]
The post Yambani kulongedza ife tidzakonze zinthu, Kabambe wauza a Chakwera appeared first on Malawi24.