A Norman Chisale omwe ndi mtsogoleri wa achinyamata mu chipani cha Democratic Progressive (DPP), yemwenso ndi wachitetezo wamkulu wa a Peter Mutharika wati mtsogoleri wawo sadakule ndipo adakali ndi mphamvu mwakuti akhonza kutsogolera dziko. A Chisale anayankhula izi ku Nyambadwe mu mzinda wa Blantyre, pamene akukonzekera kuyamba ulendo wa misonkhano yoyimayima yomwe akonza mu mzindawu. […]
The post Peter Mutharika mukuti wakula, wakulira kuti? - Chisale appeared first on Malawi 24.