Woyankhulira chipembedzo cha chisilamu Sheikh Dinala Chabulika wati dziko lino likumagawanika chifukwa cha mipingo maka ikaonetsa chidwi pa amene anthu akhonza kudzamsankha pa masankho a mtsogoleri wa dziko ndipo ati nthawi yakwana tsopano kuti atsogoleri a bungwe la Public affairs Committee (PAC) asamalandile ma udindo kuchokera kwa mtsogoleri wa dziko. Poyankhula lero mu pologamu ya […]
The post Ma Membala a PAC apewe kulandira ma udindo kuchokera kwa mtsogoleri wa dziko appeared first on Malawi 24.