Bwalo la milandu la Zomba lamasula Mayi Jenita Matiasi yemwe adagamulidwa kuti akakhale kundende zaka zisanu pa mlandu wakupha khanda losabadwa la miyezi isanu ndi itatu (8). Malingana ndi Legal Aid Bureau, Mayi Matiasi ndi nzika ya dziko la Mozambique ndipo adamangidwa chaka chino m’mwezi wa February koma anachita apilu mothandizidwa ndi Legal Aid Bureau […]
The post Mayi oganizilidwa kuti adapha khanda wamasulidwa appeared first on Malawi 24.