Sipikala wa Nyumba ya Malamulo a Catherine Gotani Hara wapereka masiku asanu ndi awiri kwa Phungu wa Blantyre City South East a Sameer Suleman, kuti afotokoze chifukwa chomwe anapitila ku nkhokwe za feteleza za SFFRFM opanda kudziwitsa akuluakulu a ofesiyo. A Suleman anapita ku SFFRFM komwe amafuna akawone ngatidi kuli feteleza, ndipo kupita kwawo Ku […]
The post A Suleman mubwere mudzafokoze chifukwa chomwe munadziwitsira dziko kuti ku SFFRFM kulibe feteleza - Hara appeared first on Malawi 24.