Wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino yemwenso ndi mtsogoleri wakale wa UTM Micheal Usi walangiza anthu kuti adzikhala mwa mtendere ndi anzawo ndipo adzigwiritsa ntchito mutu wawo potsatira zipani ponena kuti asamangolonda komwe anzawo apita mosaganizira bwino. A Usi alankhula izi kumudzi kwawo kwa Ngolowera mfumu yayikulu Chikumbu m'boma la Mulanje lero komwe anapita kukagawira […]
The post Za chipanizi nthawi zina kumaziona bwino - Usi appeared first on Malawi 24.