Itatuluka mu ligi m'chaka cha 2023, timu ya apolisi ya Blue Eagles tsopano yabweleranso mu ligi yayikulu ya mdziko muno ya TNM Super League kutsatira kukhala akatswiri mu chikho cha Chipiku Stores Central Region Football League itagonjetsa Armour Battalion 4-1 pa bwalo la ADL ku Lilongwe Lachitatu. Eagles yomwe yatsala ndi masewelo awiri kuti imalize […]
The post Tilandileni tafikanso, Blue Eagles yabweleranso mu TNM Super League appeared first on Malawi 24.