Mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera ati a Malawi adzasangalara mu gawo lachiwiri la ulamuliro wawo omwe uyambe chikachitika chisankho cha dziko cha chaka chino. A Chakwera avomereza kuti dziko lawavuta kuyendetsa maka mu zaka zisanu zomwe alamulira ndipo a Malawi ochuluka zedi amva kuwawa kwambiri mu ulamuliro umenewu. Malinga ndi a Chakwera kumva […]
The post Dziko landivuta kuyendetsa zaka zisanuzi koma mukandivotelanso, mudzananala - Chakwera appeared first on Malawi 24.