Gulu la amai la Sarah mu m'mpingo wa Living Waters International ku Bangula m'boma la Nsanje, lidakachezera odwala pa chipatala cha Kalemba mu nyengo yachikondwelero cha Khirisimisi. Malingana ndi mai Mbusa Priscilla M'bwana, chimodzi mwa utumiki wa amai a Sarah ndikuyendera komanso kuchezetsa anthu odwala. Iye ati m'chifukwa chake anachiona choyenera kudzasangalatsa odwala ku chipatalachi. […]
The post Amai a Sarah achezera odwala pa chipatala cha Kalemba appeared first on Malawi 24.