Wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino a Michael Usi alangiza anthu amene akulandira chimanga kudzera mu ndondomeko yothandiza anthu amene akusowa chakudya kuti akalandira chimanga asamale posadya moononga chifukwa ndi chochita kupatsidwa. A Usi ati kwa olandira chakudyachi adye mwa mlingo oyenera ndipo apempha kwa anthu amene ali ndi chakudya kuti athandize anzawo amene alibe […]
The post Chakudya cholandira osadya moononga - Usi appeared first on Malawi 24.