Mwana wa zaka ziwiri wamwalira m'boma la Mangochi atapsa modetsa nkhawa nyumba yomwe amakhala itayaka moto. Potsimikiza za ngoziyi, ofalitsa nkhani ku polisi ya Monkey-Bay, Alice Sichali, wati nyumbayi idayaka kamba ka mafuta a galimoto omwe amasungidwa mnyumbayi. Sichali wati izi zidachitika pa tsiku la khilisimisi pa 25 December, 2025 pa Malo ochitira malonda a […]
The post Amwalira nyumba itayaka moto appeared first on Malawi 24.