Mchitidwe okupha nsomba mosatsata malamulo ukuchulukira mnyanja ya Chilwa chifukwa cha kuchuluka kwa chiwerengero cha anthu amene amakhala mozungulira nyanjayi. Mkulu oyang'anira kaphedwe ka msomba m'boma la Zomba, Elliot Lungu wati kuchuluka kwa anthu kukukolezera mchitidwe okupha msomba mwachisawawa. Mau ake, Lungu wapempha mabungwe ndi anthu okhala mozungulira nyanja ya Chilwa kuti atenge gawo kuteteza […]
The post Kupha nsomba mosatsata malamulo kukuchulukira mnyanja ya Chirwa appeared first on Malawi 24.