Gulu la Mbadwa Zokhudzidwa ladzudzula mchitidwe ogwilitsa ntchito bungwe la ACB molakwika polipatsa uthenga opotoka ndi cholinga chofuna kuipitsilana mbiri maka pamene zipani zikupita ku misonkhano yaikulu - convention. Polakhula kwa atolankhan dzulo modzi wa akuluakulu a gululi a Fredrick Billy Malata anati Pali anthu ena omwe akugwilitsa ntchito ACB pofuna kuipitsilana mbiri maka pamene […]
The post Gulu la Mbadwa zokhudzidwa lidzudzula m'chitidwe ogwilitsa ntchito bungwe la ACB molakwika appeared first on Malawi 24.