Bwalo la milandu munzinda wa Lilongwe lagamula kuti Norman Chisale ndi mfulu pa milandu isanu ndi umodzi (6) kuphatikiza omwe anamangidwa kamba konena mau onyazitsa nduna ya za chilungamo a Titus Mvalo. A Chisale omwe anali mkulu owona za chitetezo cha mtsogoleri wa kale wa dziko lino Peter Mutharika, anamangidwa kangapo konse mbuyomu ndipo anatsekulilidwa […]
The post Norman Chisale apezeka osalakwa pa milandu yoposera isanu appeared first on Malawi 24.