Anthu asanu ndi m’modzi (6) mu nzinda wa Lilongwe, ali m’manja mwa apolisi poganizilidwa kuti anali m'gulu la omwe anagenda ma ofesi a nthambi yowona zolowa ndikutuluka m’dziko muno (DICS) pa nkhani ya ziphaso. Lachinayi masana, anthu okwiya mu nzindawu anagenda ku maofesi a nthambi ya DISC kamba kokhumudwa kuti nthambiyi ikuchedwa kuwapatsa ziphaso zawo […]
The post Anthu asanu ndi m'modzi anjatidwa pogenda ma ofesi a nthambi yowona zolowa ndi zotuluka appeared first on Malawi 24.