Omenyera ufulu wa anthu Bon Kalindo yemwe wavekedwa unyolo mowilikiza pakatipa wati zithu zambiri ndizosokonekera m'dziko muno kamba koti dziko lino linapita kwa agalu. Poyankhula mu pologalamu ya padera yomwe yaulutsidwa pa wayilesi ya Zodiak Lachiwiri madzulo, Kalindo wati atsogoleri onse omwe alamulirapo dziko lino anayesa kuyika patsogolo umoyo wa anthu zomwe ati pano sizikuchitika. […]
The post Dziko lapita kwa agalu – watelo Kalindo appeared first on Malawi 24.