Dalitso Kabambe yemwe wangolowa kumene United Transformation Movement (UTM) kuchokera ku chipani cha Democratic Progressive (DPP), wati chipanichi chiyembekeze kuti chilandira alendo ankhaninkhani kuchokera ku zipani zina. Kabambe yemwe adali mkulu wa kale wa banki yaikulu ya Reserve wayankhula izi pomwe lero walandilidwa mchipani cha UTM kudzera pa msonkhano omwe wachitika pa Masambanjati m'boma la […]
The post Kubwera khwimbi ku UTM – watelo Kabambe appeared first on Malawi 24.