Sibongire Mnzinyathi yemwe ndi mkulu ozenga milandu ku Gauteng Province m’dziko la South Africa wauza bwalo la milandu kuti palibe kampani ya Mneneri Shepherd Bushiri ndi nkazi wake Mary yomwe inalandira ndalama zobedwa. Izi zadziwika pomwe lero Lolemba ma loya a Bushiri kuphatikizapo Annellen Van Den Heever, anapitilira kufunsa mafuso a Mnzinyathi molingana ndi umboni […]
The post Mboni yati Bushiri sadalandire ndalama zobedwa appeared first on Malawi 24.