Patadutsa maola oposa 24 apolisi chimangileni mkozi wa nyimbo, Chiyanjano Mbeza pa mlandu omwe sukudziwika, achibale ake ati mpaka pano sakudziwabe polisi yomwe m'bale wawoyu akusungidwa. Mbeza yemwe amajambula nyimbo munzinda wa Blantyre, anamangidwa madzulo a Lolemba sabata ino pa zifukwa zomwe mpaka pano sizikudziwika. Ganizani Mbeza yemwe ndi mchimwene wake wa Chiyanjano, Lachiwiri anauza […]
The post Abale sakudziwabe komwe kuli Chiyanjano Mbeza appeared first on Malawi 24.