Khonsolo ya nzinda wa Blantyre yatsutsa mphekesera zomwe zikumveka kuti yagulitsa nsika wa Kamba kwa mponda matiki wina wa chimwenye. Sabata yomwe ikungothayi kwakhala kukumveka manong’onong’o kuti khonsolo ya nzinda wa Blantyre yagulitsa nsika wa Kamba kwa munthu wina yemwe akuti akufuna kupangapo chitukuko china. Tsamba lino linavetsedwa kuti ochita malonda munsikawu anagwirizana kuti apite […]
The post Sitinagulitse nsika wa Kamba – yatsutsa khonsolo ya nzinda wa Blantyre appeared first on Malawi 24.