Akatswiri ozukuta bwino nkhani za ndale mdziko muno a Chimwemwe Tsitsi ndi a Victor Chipofya ati zipani zandale zikapitilira kutayiilira kuti zili ndi madela omwe amawati ndi amphamvu zililira kuutsi pa zotsatira za zisankho. A Tsitsi ati zipani ziphunzire kuti pamene zili ndi dela lomwe kumachokera owatsatira ambiri sakuyenera kutayilira kuti mzachidziwikire kuti adzipambana pa […]
The post Kulekelera kudzivulazabe zipani pa masankho appeared first on Malawi 24.