Mayi wa zaka 40 m'boma la Kasungu ali m’manja mwa apolisi atapha ana anayi powamenya Lolemba pa 22 July 2024. Wofalitsa nkhani za apolisi m’bomali Joseph Kachikho azindikira mayi oganizilidwayu ngati Ireen Banda. Mayi Banda, akuganizilidwa kuti Lolemba lapitali wapha Funny Banda wa chaka chimodzi ndii miyezi isanu, Richard Nkhata wa zaka zisanu ndi zitatu, […]
The post Mai apha ana anayi pofuna kuwachotsa mizimu yoipa appeared first on Malawi 24.