Pomwe njala yafika posautsa m'boma la Machinga, Mfumu Yayikulu Nchinguza ya m'bomali yanena kuti pa tsiku ikulandila madando osachepera asanu ndi awiri okhudza abambo omwe akuthawa mabanja awo kuthawira mdziko la Mozambique, chifukwa cha njala yomwe yavuta m'derali. Malingana ndi Mfumuyi, abambowa sakumabwelera pa kutha kwa nthawi, akapita kukasaka maganyu m'dziko la Mozambique, lomwe lachita […]
The post Njala yavuta ku Machinga, azibambo akuthawa mabanja awo appeared first on Malawi 24.