Pamene ntchito yokonza miseu ina ya mzinda wa Lilongwe idakapitilira, Khonsolo ya mzindawu yati ikhala ikutseka miseu ina monga wa CH 2+ 950 kukafika 2+980 (pafupi ndi Galaxy shop) kuyambila Lolemba pa 25 March, 2024 mpaka Lachisanu pa 6 April, 2024. Malingana ndi chikalata chomwe wasainila ndi Bwanankubwa wa khonsoloyi, Dr McCloud Kam'manja, onse ochita […]
The post Khonsolo ya mzinda wa Lilongwe yati itseka miseu ina mzindawu appeared first on Malawi 24.