Nthambi ya zaumoyo ku khonsolo ya boma la Neno yati pofika Lolemba pa 25 March, 2024, chiwerengero cha anthu omwe apezeka ndi nthenda ya Rubella chakwera ndipo chafika pa anthu 23. Lolemba pa 25 March, 2024 thambi ya zaumoyo m’bomali yatulutsa chikalata chopeleka tsatanetsatane wa mmene zinthu zilili m’bomali potsati kubuka kwa matenda a Rubella […]
The post Chiwerengero cha odwala Rubella chakwera ku Neno appeared first on Malawi 24.