Unduna wa Zaumoyo wati m’boma la Neno kwabuka nthenda yotchedwa Rubella yomwe yagwira anthu khumi ndi m’modzi. Izi ndi malingana ndi kalata yomwe undunawu watulutsa lachisanu pa 23 March, 2024 yomwe asayinira ndi Dr Samson Mndolo omwe ndi mlembi wamkulu mu unduna wa zaumoyo Undunawu wati pa 15 March chaka chino unalandira malipoti kuchokera ku […]
The post Ku Neno kwabuka nthenda ya Rubella appeared first on Malawi 24.